Lero pa 26 March 2025, Amayi a Mula Deanary, momwe St Kizito Parish ndi imodzi mwa ma parish mudeaneryi, anakadzala mitengo ku Mkwichi Primary School Area 47.
Kubwezeretsa chilengedwe podzala mitengo ndi imodzi mwa zolinga za bungwe la amayi mu deaneryi.